MFUMU ya ULEMELERO | Gawo la sewero 62/70 | Rex of GLORY | Chichewa
Gawo la sewero 62: Mpulumutsi-Mfumu
Pokwaniritsa dongosolo la chipulumutso cha Mulungu, Ambuye Yesu anachititsidwa manyazi ndi zomwe tchimo limabweretsa. Anatembereredwa m’malo mwa ife. Anatenga chilango chomwe chimatiyenera ife.
Ulendo wa mu Malemba a Aneneri umakuitanani inu kuti mukumane ndi Mfumu ya dziko komanso kumvetsa dongosolo lake lopulumutsa omutsatira oukira kuchokera ku ufumu wa mdima ndi kuwayenereza kukhala mu kuunika kwa Ufumu wake Muyaya.
Mofotokozeredwa kwa nzeru ndi zithunzi zokongongola kanema uyu ndi oyenera kwa anthu a dziko lonse ndi misikhu yonse.
Kanema yonse ndi ya mphindi 222, ndime 15, ndi magawo akulu awiri.
Gawo 1. Chipangano cha Kale: Mfumu kufotokozera dongosolo lake (Ndime 1-8)
Gawo 2. Chipangano cha Tsopano: Mfumu Ikwanilitsa Dongosolo lake (Ndime 9-15)
© 2020 ROCK International https://Rex-of-glory.com
Scene 62: The Savior-Rex
To fulfill God’s rescue plan, the Lord Jesus felt the shame sin brings. He was cursed inwards our place. He took the punishment we deserve.
This journeying into the Scriptures of the prophets invites you to come across the 1 true God and understand His plan to rescue His rebellious subjects from the kingdom of darkness and qualify them to live with Him forever inwards His kingdom of calorie-free. With its thought-provoking narrative and inspired mix of animation and live video, this film is for a worldwide audience.
The full film is 222 minutes, composed of 70 Scenes grouped inwards 15 episodes, and divided into two main parts:
component 1. Old Testament: The Rex Foretells His Plan {Episodes 1-8}
component 2. New Testament: The Rex Fulfills His Plan {Episodes 9-15}
© 2020 ROCK International https://Rex-of-glory.com